Danieli 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Inu munaona mtengo umene unakula kwambiri ndipo unakhala wamphamvu kwambiri. Mtengowo unatalika mpaka kufika kumwamba ndipo unali kuoneka padziko lonse lapansi.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:20 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 32 Nsanja ya Olonda,9/1/2007, ptsa. 18-19
20 “‘Inu munaona mtengo umene unakula kwambiri ndipo unakhala wamphamvu kwambiri. Mtengowo unatalika mpaka kufika kumwamba ndipo unali kuoneka padziko lonse lapansi.+