Danieli 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Masamba ake anali okongola ndipo unali ndi zipatso zambiri. Mumtengomo munali zakudya zokwanira chamoyo chilichonse. Nyama zakutchire zinali kukhala pansi pake.+ Mbalame zam’mlengalenga zinali kukhala panthambi zake. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:21 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 32
21 Masamba ake anali okongola ndipo unali ndi zipatso zambiri. Mumtengomo munali zakudya zokwanira chamoyo chilichonse. Nyama zakutchire zinali kukhala pansi pake.+ Mbalame zam’mlengalenga zinali kukhala panthambi zake.