-
Danieli 6:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Poona zimenezi, nduna zapamwamba ndi masatarapi aja nthawi zonse anali kufunafuna chomunamizira Danieli pa kayendetsedwe kake ka zinthu mu ufumuwo.+ Koma iwo sanapeze chifukwa chilichonse chomunamizira kapena chinthu chilichonse chachinyengo chimene anachita, pakuti iye anali wokhulupirika. Iwo anapeza kuti Danieli sanali kunyalanyaza kanthu kapena kuchita zachinyengo zilizonse.+
-