Danieli 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mfumuyo itangomva mawu amenewa, inakhumudwa kwambiri+ ndipo inayamba kuganiza za mmene ingapulumutsire Danieli.+ Inakhala ikufunafuna njira yomupulumutsira mpaka dzuwa linalowa. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:14 Ulosi wa Danieli, tsa. 120
14 Mfumuyo itangomva mawu amenewa, inakhumudwa kwambiri+ ndipo inayamba kuganiza za mmene ingapulumutsire Danieli.+ Inakhala ikufunafuna njira yomupulumutsira mpaka dzuwa linalowa.