Danieli 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamapeto pake, amuna amphamvu amenewa anapita kwa mfumu ali chigulu ndipo anaiuza kuti: “Inu mfumu, mukudziwa kuti malamulo a Amedi ndi Aperisiya amanena kuti lamulo lililonse+ lokhazikitsidwa ndi mfumu siliyenera kusinthidwa.”+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:15 Ulosi wa Danieli, tsa. 120
15 Pamapeto pake, amuna amphamvu amenewa anapita kwa mfumu ali chigulu ndipo anaiuza kuti: “Inu mfumu, mukudziwa kuti malamulo a Amedi ndi Aperisiya amanena kuti lamulo lililonse+ lokhazikitsidwa ndi mfumu siliyenera kusinthidwa.”+