Danieli 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako mfumu inapita kunyumba yake yachifumu. Usiku umenewo mfumuyo inasala kudya+ ndipo sanaiimbire nyimbo ndi zipangizo zoimbira, komanso sinathe kugona tulo.+
18 Kenako mfumu inapita kunyumba yake yachifumu. Usiku umenewo mfumuyo inasala kudya+ ndipo sanaiimbire nyimbo ndi zipangizo zoimbira, komanso sinathe kugona tulo.+