Danieli 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye amapulumutsa ndi kulanditsa anthu ake,+ ndipo amachita zizindikiro komanso zinthu zodabwitsa kumwamba+ ndi padziko lapansi,+ moti wapulumutsa Danieli kwa mikango.”
27 Iye amapulumutsa ndi kulanditsa anthu ake,+ ndipo amachita zizindikiro komanso zinthu zodabwitsa kumwamba+ ndi padziko lapansi,+ moti wapulumutsa Danieli kwa mikango.”