Danieli 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Tsopano ineyo Danieli, ndinavutika kwambiri mumtima chifukwa cha zimenezi ndipo ndinachita mantha ndi masomphenya amene ndinaona.+
15 “Tsopano ineyo Danieli, ndinavutika kwambiri mumtima chifukwa cha zimenezi ndipo ndinachita mantha ndi masomphenya amene ndinaona.+