Danieli 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Nkhani imeneyi yathera pamenepa. Tsopano ineyo Danieli, ndinachita mantha kwambiri moti ndinakhala ngati ndakomoka. Koma nkhaniyi ndinaisunga mumtima mwanga.”+
28 “Nkhani imeneyi yathera pamenepa. Tsopano ineyo Danieli, ndinachita mantha kwambiri moti ndinakhala ngati ndakomoka. Koma nkhaniyi ndinaisunga mumtima mwanga.”+