Danieli 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 M’chaka choyamba cha Dariyo mwana wa Ahasiwero,+ wa mtundu wa Amedi,+ amene anaikidwa kukhala mfumu ya ufumu wa Akasidi,+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:1 Ulosi wa Danieli, tsa. 181
9 M’chaka choyamba cha Dariyo mwana wa Ahasiwero,+ wa mtundu wa Amedi,+ amene anaikidwa kukhala mfumu ya ufumu wa Akasidi,+