Danieli 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ife tachimwa,+ talakwa, tachita zinthu zoipa ndipo takupandukirani.+ Tapatuka ndiponso tasiya malamulo anu ndi zigamulo zanu.+
5 Ife tachimwa,+ talakwa, tachita zinthu zoipa ndipo takupandukirani.+ Tapatuka ndiponso tasiya malamulo anu ndi zigamulo zanu.+