Danieli 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sitinamvere atumiki anu aneneri,+ amene analankhula m’dzina lanu kwa mafumu athu, akalonga athu, makolo athu, ndi anthu onse a m’dziko lathu.+
6 Sitinamvere atumiki anu aneneri,+ amene analankhula m’dzina lanu kwa mafumu athu, akalonga athu, makolo athu, ndi anthu onse a m’dziko lathu.+