Danieli 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Tsopano inu Yehova Mulungu wathu, amene munatulutsa anthu anu m’dziko la Iguputo ndi dzanja lamphamvu,+ amenenso munadzipangira dzina kufikira lero,+ ife tachimwa,+ tachita zinthu zoipa. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:15 Ulosi wa Danieli, ptsa. 183-184
15 “Tsopano inu Yehova Mulungu wathu, amene munatulutsa anthu anu m’dziko la Iguputo ndi dzanja lamphamvu,+ amenenso munadzipangira dzina kufikira lero,+ ife tachimwa,+ tachita zinthu zoipa.