Danieli 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 inde, pamene ndinali kulankhula zimenezi m’pemphero, munthu uja Gabirieli,+ amene ndinamuona m’masomphenya nditatopa kwambiri poyamba paja,+ ndinamuona akubwera kwa ine pa nthawi yopereka nsembe yamadzulo, yoperekedwa ngati mphatso.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:21 Nsanja ya Olonda,9/1/2007, tsa. 20 Ulosi wa Danieli, ptsa. 184-185
21 inde, pamene ndinali kulankhula zimenezi m’pemphero, munthu uja Gabirieli,+ amene ndinamuona m’masomphenya nditatopa kwambiri poyamba paja,+ ndinamuona akubwera kwa ine pa nthawi yopereka nsembe yamadzulo, yoperekedwa ngati mphatso.+