Danieli 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene unali kuyamba kupemphera ndinalandira uthenga, choncho ndabwera kudzakufotokozera za uthengawo chifukwa iwe ndiwe munthu wokondedwa kwambiri.+ Tsopano khala tcheru,+ ndipo umvetsetse zinthu zimene ukuona. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:23 Nsanja ya Olonda,9/1/2007, tsa. 20 Ulosi wa Danieli, ptsa. 7, 184-186
23 Pamene unali kuyamba kupemphera ndinalandira uthenga, choncho ndabwera kudzakufotokozera za uthengawo chifukwa iwe ndiwe munthu wokondedwa kwambiri.+ Tsopano khala tcheru,+ ndipo umvetsetse zinthu zimene ukuona.