Hoseya 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Efuraimu akalankhula, anthu anali kunjenjemera. Iye anali wolemekezeka mu Isiraeli,+ koma anapezeka ndi mlandu wolambira Baala+ ndipo anafa.+
13 “Efuraimu akalankhula, anthu anali kunjenjemera. Iye anali wolemekezeka mu Isiraeli,+ koma anapezeka ndi mlandu wolambira Baala+ ndipo anafa.+