Hoseya 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo adzakhalanso mumthunzi wake.+ Adzabzala mbewu ndipo adzaphuka ngati mpesa.+ Dzina lawo lidzakumbukiridwa ngati vinyo wa ku Lebanoni.
7 Iwo adzakhalanso mumthunzi wake.+ Adzabzala mbewu ndipo adzaphuka ngati mpesa.+ Dzina lawo lidzakumbukiridwa ngati vinyo wa ku Lebanoni.