Hoseya 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndani ali ndi nzeru kuti amvetse zinthu zimenezi?+ Wochenjera ndani kuti adziwe zimenezi?+ Pakuti njira za Yehova ndi zowongoka+ ndipo anthu olungama ndi amene adzayendamo,+ koma olakwa adzapunthwa m’njira zimenezo.+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:9 Tsiku la Yehova, ptsa. 87-88 Nsanja ya Olonda,11/15/2005, tsa. 31
9 Ndani ali ndi nzeru kuti amvetse zinthu zimenezi?+ Wochenjera ndani kuti adziwe zimenezi?+ Pakuti njira za Yehova ndi zowongoka+ ndipo anthu olungama ndi amene adzayendamo,+ koma olakwa adzapunthwa m’njira zimenezo.+