Amosi 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pali mdani amene wazungulira dziko lonse+ ndipo ameneyo adzakukhalitsa wopanda mphamvu ndipo adzafunkha nsanja zako zokhalamo.’+
11 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pali mdani amene wazungulira dziko lonse+ ndipo ameneyo adzakukhalitsa wopanda mphamvu ndipo adzafunkha nsanja zako zokhalamo.’+