Yona 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho anamufunsa kuti: “Tiuze, ndani wachititsa kuti tsoka limeneli litigwere?+ Umagwira ntchito yanji ndipo ukuchokera kuti? Kwanu n’kuti ndipo ndiwe wa mtundu uti?”
8 Choncho anamufunsa kuti: “Tiuze, ndani wachititsa kuti tsoka limeneli litigwere?+ Umagwira ntchito yanji ndipo ukuchokera kuti? Kwanu n’kuti ndipo ndiwe wa mtundu uti?”