Yona 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti:“Pamene ndinali m’masautso ndinaitana Yehova,+ ndipo anandiyankha.+Ndinafuula kupempha thandizo ndili m’Manda* akuya.+Ndipo inu munamva mawu anga.+ Yona Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:2 Nsanja ya Olonda,5/15/1996, ptsa. 25-264/15/1989, tsa. 31 Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 85
2 kuti:“Pamene ndinali m’masautso ndinaitana Yehova,+ ndipo anandiyankha.+Ndinafuula kupempha thandizo ndili m’Manda* akuya.+Ndipo inu munamva mawu anga.+