Yona 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndinatsikira m’tsinde mwenimweni mwa mapiri.Zotsekera za dziko lapansi zinanditsekereza kuti ndikhale komweko mpaka kalekale.*Koma inu Yehova Mulungu wanga, munanditulutsa m’dzenje ndili wamoyo.+ Yona Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:6 Nsanja ya Olonda,5/15/1996, tsa. 26
6 Ndinatsikira m’tsinde mwenimweni mwa mapiri.Zotsekera za dziko lapansi zinanditsekereza kuti ndikhale komweko mpaka kalekale.*Koma inu Yehova Mulungu wanga, munanditulutsa m’dzenje ndili wamoyo.+