Habakuku 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Choncho lamulo latha mphamvu ndipo anthu sakuchitanso chilungamo.+ Chilungamo chapotozedwa chifukwa anthu oipa akupondereza anthu olungama.+ Habakuku Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:4 Nsanja ya Olonda,2/1/2000, tsa. 9
4 “Choncho lamulo latha mphamvu ndipo anthu sakuchitanso chilungamo.+ Chilungamo chapotozedwa chifukwa anthu oipa akupondereza anthu olungama.+