Habakuku 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, kodi mwapsera mtima mitsinje?+ Kodi mkwiyo wanu wayakira nyanja+ pamene inu munakwera pamahatchi anu?+ Magaleta anu anabweretsa chipulumutso.+
8 Inu Yehova, kodi mwapsera mtima mitsinje?+ Kodi mkwiyo wanu wayakira nyanja+ pamene inu munakwera pamahatchi anu?+ Magaleta anu anabweretsa chipulumutso.+