Habakuku 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munapita kuti mukapulumutse anthu anu,+ kuti mukapulumutse wodzozedwa wanu. Munaphwanyaphwanya mtsogoleri wa nyumba ya wochimwa.+ Nyumbayo inafafanizidwa mpaka kudenga moti maziko a nyumbayo anaonekera.+ [Seʹlah.] Habakuku Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:13 Nsanja ya Olonda,11/15/2007, tsa. 102/1/2000, tsa. 225/15/1989, tsa. 24
13 Munapita kuti mukapulumutse anthu anu,+ kuti mukapulumutse wodzozedwa wanu. Munaphwanyaphwanya mtsogoleri wa nyumba ya wochimwa.+ Nyumbayo inafafanizidwa mpaka kudenga moti maziko a nyumbayo anaonekera.+ [Seʹlah.]