Zekariya 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Turo anamanga chiunda chomenyerapo nkhondo.* Anadziunjikira siliva wochuluka ngati dothi ndiponso golide wochuluka ngati matope a m’misewu.+
3 Turo anamanga chiunda chomenyerapo nkhondo.* Anadziunjikira siliva wochuluka ngati dothi ndiponso golide wochuluka ngati matope a m’misewu.+