Zekariya 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zidzakhala zoonekeratu kuti Yehova ali ndi anthu ake,+ ndipo muvi wake udzathamanga ngati mphezi.+ Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa adzaliza lipenga lanyanga ya nkhosa,+ ndipo adzapita ndi mphepo yamkuntho ya kum’mwera.+
14 Zidzakhala zoonekeratu kuti Yehova ali ndi anthu ake,+ ndipo muvi wake udzathamanga ngati mphezi.+ Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa adzaliza lipenga lanyanga ya nkhosa,+ ndipo adzapita ndi mphepo yamkuntho ya kum’mwera.+