Zekariya 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amene anazigula anazipha+ koma sanaimbidwe mlandu.+ Amene akuzigulitsa+ akunena kuti: “Yehova atamandike pamene ine ndikupeza chuma.”+ Abusa ake sazichitira chifundo ngakhale pang’ono.’+
5 Amene anazigula anazipha+ koma sanaimbidwe mlandu.+ Amene akuzigulitsa+ akunena kuti: “Yehova atamandike pamene ine ndikupeza chuma.”+ Abusa ake sazichitira chifundo ngakhale pang’ono.’+