Zekariya 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Panganolo linasweka pa tsiku limenelo. Mwa njira imeneyi, nkhosa zosautsika+ zimene zinali kundiona+ zinadziwa kuti zimene ndachitazo n’zimene Yehova ananena.
11 Panganolo linasweka pa tsiku limenelo. Mwa njira imeneyi, nkhosa zosautsika+ zimene zinali kundiona+ zinadziwa kuti zimene ndachitazo n’zimene Yehova ananena.