Zekariya 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Pa tsiku limenelo,+ kudzakumbidwa chitsime+ kuti a m’nyumba ya Davide ndi anthu okhala mu Yerusalemu adzayeretsedwe ku machimo+ ndi ku zinthu zawo zonyansa.+
13 “Pa tsiku limenelo,+ kudzakumbidwa chitsime+ kuti a m’nyumba ya Davide ndi anthu okhala mu Yerusalemu adzayeretsedwe ku machimo+ ndi ku zinthu zawo zonyansa.+