Zekariya 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Zikadzatero, aneneri azidzachita manyazi pa tsiku limenelo.+ Azidzachita manyazi ndi masomphenya awo pamene akulosera. Sadzavalanso chovala chapadera chaubweya+ kuti anamize anthu.
4 “Zikadzatero, aneneri azidzachita manyazi pa tsiku limenelo.+ Azidzachita manyazi ndi masomphenya awo pamene akulosera. Sadzavalanso chovala chapadera chaubweya+ kuti anamize anthu.