19 Chotero aliyense wophwanya+ lililonse la malamulo aang’ono awa ndi kuphunzitsa anthu kuphwanya malamulowo, adzakhala ‘wosayenera kulowa’ mu ufumu wakumwamba.+ Koma aliyense wotsatira ndi kuphunzitsa malamulowa,+ ameneyo adzakhala ‘woyenera kulowa’+ mu ufumu wakumwamba.