Mateyu 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kapena ungauze bwanji m’bale wako kuti, ‘Taima ndikuchotse kachitsotso m’diso lako,’ pamene iwe m’diso lako muli mtanda wa denga la nyumba?+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:4 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, ptsa. 9-10
4 Kapena ungauze bwanji m’bale wako kuti, ‘Taima ndikuchotse kachitsotso m’diso lako,’ pamene iwe m’diso lako muli mtanda wa denga la nyumba?+