Mateyu 7:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiye kunagwa chimvula champhamvu ndipo madzi anasefukira. Kenako chimphepo chinafika n’kuwomba nyumbayo+ moti inagwa, ndipo kugwa kwake kunali kwakukulu.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:27 Nsanja ya Olonda,11/1/2008, ptsa. 29-312/15/2008, ptsa. 31-32
27 Ndiye kunagwa chimvula champhamvu ndipo madzi anasefukira. Kenako chimphepo chinafika n’kuwomba nyumbayo+ moti inagwa, ndipo kugwa kwake kunali kwakukulu.”+