Mateyu 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yesu anatumiza atumwi 12 amenewa, ndipo anawapatsa malangizo awa:+ “Musapite mumsewu wa anthu a mitundu ina, ndipo musalowe mumzinda wa Asamariya.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:5 Nsanja ya Olonda,8/15/1987, tsa. 30
5 Yesu anatumiza atumwi 12 amenewa, ndipo anawapatsa malangizo awa:+ “Musapite mumsewu wa anthu a mitundu ina, ndipo musalowe mumzinda wa Asamariya.+