Mateyu 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma akakuperekani kumeneko, musade nkhawa za mmene mukalankhulire kapena zimene mukanene. Mudzapatsidwa nthawi yomweyo zoti mulankhule,+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:19 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),9/2021, ptsa. 24-25
19 Koma akakuperekani kumeneko, musade nkhawa za mmene mukalankhulire kapena zimene mukanene. Mudzapatsidwa nthawi yomweyo zoti mulankhule,+