Mateyu 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komanso munthu adzapereka m’bale+ wake ku imfa, ndipo bambo adzapereka mwana wake. Ana adzaukira makolo awo ndipo adzawaphetsa.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:21 Yesu—Ndi Njira, tsa. 124 Nsanja ya Olonda,5/15/1991, tsa. 31
21 Komanso munthu adzapereka m’bale+ wake ku imfa, ndipo bambo adzapereka mwana wake. Ana adzaukira makolo awo ndipo adzawaphetsa.+