Mateyu 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Zimene ndimakuuzani mu mdima, muzinene poyera, ndipo zimene mumamva anthu akunong’onezana, muzilalikire pamadenga.+
27 Zimene ndimakuuzani mu mdima, muzinene poyera, ndipo zimene mumamva anthu akunong’onezana, muzilalikire pamadenga.+