Mateyu 10:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Aliyense wopulumutsa moyo wake adzautaya, ndipo wotaya moyo wake chifukwa cha ine adzaupeza.+