Mateyu 10:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Amene wakulandirani walandiranso ine, ndipo amene walandira ine walandiranso amene anandituma.+