Mateyu 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene ophunzira a Yohane anali kubwerera, Yesu anayamba kuuza khamu la anthulo za Yohane kuti: “Kodi munapita m’chipululu kukaona chiyani?+ Kodi munapita kukaona bango logwedezeka ndi mphepo?+
7 Pamene ophunzira a Yohane anali kubwerera, Yesu anayamba kuuza khamu la anthulo za Yohane kuti: “Kodi munapita m’chipululu kukaona chiyani?+ Kodi munapita kukaona bango logwedezeka ndi mphepo?+