Mateyu 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nangano n’chifukwa chiyani munapita makamaka? Kukaona mneneri kapena? Inde, ndikukuuzani, woposadi mneneri.+
9 Nangano n’chifukwa chiyani munapita makamaka? Kukaona mneneri kapena? Inde, ndikukuuzani, woposadi mneneri.+