Mateyu 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komabe, ngati mukanamvetsa tanthauzo la mawu akuti, ‘Ndikufuna chifundo,+ osati nsembe,’+ simukanaweruza anthu osalakwa.
7 Komabe, ngati mukanamvetsa tanthauzo la mawu akuti, ‘Ndikufuna chifundo,+ osati nsembe,’+ simukanaweruza anthu osalakwa.