Mateyu 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako anauza munthuyo kuti: “Tambasula dzanja lako.” Iye analitambasuladi, ndipo linakhalanso bwinobwino ngati linzake.+
13 Kenako anauza munthuyo kuti: “Tambasula dzanja lako.” Iye analitambasuladi, ndipo linakhalanso bwinobwino ngati linzake.+