Mateyu 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Podziwa maganizo awo,+ iye anawauza kuti: “Ufumu uliwonse wogawanika umatha,+ ndipo mzinda uliwonse kapena nyumba yogawanika siikhalitsa. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:25 Nsanja ya Olonda,9/1/2002, ptsa. 10-12
25 Podziwa maganizo awo,+ iye anawauza kuti: “Ufumu uliwonse wogawanika umatha,+ ndipo mzinda uliwonse kapena nyumba yogawanika siikhalitsa.