Mateyu 12:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Anthu a ku Nineve adzaimirira pa chiweruzo limodzi ndi m’badwo uwu+ ndipo adzautsutsa,+ chifukwa iwo analapa atamva ulaliki wa Yona.+ Koma tsopano wina woposa Yona ali pano. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:41 Nsanja ya Olonda,5/15/1996, tsa. 28
41 Anthu a ku Nineve adzaimirira pa chiweruzo limodzi ndi m’badwo uwu+ ndipo adzautsutsa,+ chifukwa iwo analapa atamva ulaliki wa Yona.+ Koma tsopano wina woposa Yona ali pano.