Mateyu 12:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 “Mzimu wonyansa ukatuluka mwa munthu, umadutsa m’malo ouma kufunafuna malo okhala, ndipo supeza alionse.+
43 “Mzimu wonyansa ukatuluka mwa munthu, umadutsa m’malo ouma kufunafuna malo okhala, ndipo supeza alionse.+