Mateyu 12:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ali mkati molankhula ndi khamu la anthulo, kunabwera mayi ake ndi abale ake.+ Iwo anaima panja kufuna kuti alankhule naye.
46 Ali mkati molankhula ndi khamu la anthulo, kunabwera mayi ake ndi abale ake.+ Iwo anaima panja kufuna kuti alankhule naye.