Mateyu 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ulosi wa Yesaya ukukwaniritsidwa pa iwowa, umene umati, ‘Kumva, mudzamva ndithu, koma osazindikira tanthauzo lake. Kuona, mudzaona ndithu, koma osazindikira.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:14 Nsanja ya Olonda,4/1/1987, tsa. 8
14 Ulosi wa Yesaya ukukwaniritsidwa pa iwowa, umene umati, ‘Kumva, mudzamva ndithu, koma osazindikira tanthauzo lake. Kuona, mudzaona ndithu, koma osazindikira.+