Mateyu 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu aliyense akamva mawu a ufumu koma osazindikira tanthauzo lake, woipayo+ amabwera n’kukwatula zomwe zafesedwa mumtima wa munthuyo. Izi ndi zofesedwa m’mbali mwa msewu zija. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:19 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 78-80 Nsanja ya Olonda,2/1/2003, ptsa. 8-98/1/1993, tsa. 19
19 Munthu aliyense akamva mawu a ufumu koma osazindikira tanthauzo lake, woipayo+ amabwera n’kukwatula zomwe zafesedwa mumtima wa munthuyo. Izi ndi zofesedwa m’mbali mwa msewu zija.
13:19 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 78-80 Nsanja ya Olonda,2/1/2003, ptsa. 8-98/1/1993, tsa. 19